| Bullets ikumananso ndi Manoma mawa |
MAWA kulinso masewero a nkhodzo za pusi pamene matimu a MTL Wanderers ndi Big Bullets akukumananso pa bwalo la za masewero la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre.
Masewerowo... |
| |
|
| TIKAMBE ZA EDZI: Sabata lokumbukira za Edzi lithandiza kwenikweni |
NDIRI ndi chikhulupiliro kuti chaka chatha nkhani imeneyi ndidakambaponso powunikira ubwino woyezetsa magazi ndi kudziwa zotsatira ngati munthu ali... |
| |
|
| Timu ya VTC Thunders iteteza chikho cha Old Mutual |
TIMU ya VTC Thunders idateteza chikho cha masewero a volebo omwe imathandiza ndi kampani ya Old Mutual itangonjetsa timu ya VTC Veterans ndi zigoli... |
| |
|
| Apempha mabungwe athandize asilikali odwala Edzi |
MKULU woyanga’anira za matenda a Edzi m’malo a asilikali a Cobbe Baracks m’boma la Zomba a Joseph Mdzinga adapempha mabungwe onse akufuna kwabwino... |
| |
|
| ‘Tidzipereka kulimbikitsa maphunziro a ana amasiye’ |
BUNGWE lothandiza ana amasiye la Carlos Cepeda Foundation lati lizipereka poyesetsa kutukula maphunziro a ana amasiye m’dziko muno pothandiza kupereka... |
| |
|